Aroma 5:12 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Cifukwa cace, monga ucimo unalowa m'dziko lapansi mwa munthu mmodzi, ndi imfa mwa ucimo; cotero imfa inafikira anthu onse, cifukwa kuti onse anacimwa.

Aroma 5

Aroma 5:11-21