Aroma 5:10 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pakuti ngati, pokhala ife adani ace, tinayanjanitsidwa ndi Mulungu mwa imfa ya Mwana wace, makamaka ndithu, popeza ife tayanjanitsidwa, tidzapulumuka ndi moyo wace.

Aroma 5

Aroma 5:9-14