Aroma 4:13 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pakuti lonjezo lakuti iye adzakhala wolowanyumba wa dziko lapansi silinapatsidwa kwa Abrahamu ndi kwa mbeu yace mwa Lamulo, koma mwa cilungamo ca cikhulupiriro.

Aroma 4

Aroma 4:11-21