Aroma 3:4 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Msatero ai. Koma Mulungu akhale woona, ndimo anthu onse akhale onama; monga kwalembedwa,Kuti Inu mukayesedwe wolungama m'maneno anu,Ndi kuti mukalakike m'mene muweruzidwa.

Aroma 3

Aroma 3:3-8