Aroma 3:19 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo tidziwa kuti zinthu ziri zonse cizinena cilamulo cizilankhulira iwo ali naco cilamulo; kuti pakamwa ponse patsekedwe, ndi dziko lonse lapansi litsutsidwe ndi Mulungu;

Aroma 3

Aroma 3:16-29