Aroma 2:29 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

koma Myuda ndiye amene akhala wotere mumtima; ndipo mdulidwe uli wa mtima, mumzimu, si m'malembo ai; kuyamika kwace sikucokera kwa anthu, koma kwa Mulungu.

Aroma 2

Aroma 2:21-29