Aroma 16:23 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Gayo, mwini nyumba wolandira ine, ndi Eklesia yense wa Ambuye, akulankhulani inu. Erasto, ndiye woyang'anira mudzi, akulankhulani inu, ndiponso Kwarto mbaleyo.

Aroma 16

Aroma 16:20-27