Aroma 15:5 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Mulungu wa cipiriro ndi wa citonthozo apatse inu kuti mukhale ndi mtima umodzi wina ndi mnzace, monga mwa Kristu Yesu;

Aroma 15

Aroma 15:1-8