Aroma 15:31-33 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

31. kuti ndikapulumutsidwe kwa osamvera aja a ku Yudeya; ndi kuti utumiki wanga wa ku Yerusalemu ukhale wolandiridwa bwino ndi oyera mtima;

32. 6 kuti ndi cimwemwe ndikadze kwa inu mwa cifuno ca Mulungu, ndi kupumula pamodzi ndi inu.

33. Ndipo 7 Mulungu wa mtendere akhale ndi inu nonse. Amen.

Aroma 15