Aroma 15:16 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

kuti ndikhale mtumiki wa Yesu Kristu kwa anthu amitundu, wakutumikira Uthenga Wabwino wa Mulungu, kuti kupereka kwace kwa anthu amitundu kulandirike, koyeretsedwa ndi Mzimu Woyera.

Aroma 15

Aroma 15:6-22