Aroma 14:4 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndani iwe wakuweruza mnyamata wa mwini wace? iye aimirira kapena kugwa kwa mbuye wace wa mwini yekha. Ndipo adzaimiritsidwa; pakuti Ambuye ali wamphamvu kumuimiritsa.

Aroma 14

Aroma 14:1-9