Aroma 14:17 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pakuti ufumu wa Mulungu sukhala cakudya ndi cakumwa, koma cilungamo, ndi mtendere, ndi cimwemwe mwa Mzimu Woyera.

Aroma 14

Aroma 14:13-20