Aroma 14:15 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma ngati iwe wacititsa mbale wako cisoni ndi cakudya, pamenepo ulibe kuyendayendanso ndi cikondano. Usamuononga ndi cakudya cako, iye amene Kristu adamfera.

Aroma 14

Aroma 14:13-23