Aroma 12:19-21 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

19. Musabwezere coipa, okondedwa, koma patukani pamkwiyo; pakuti kwalembedwa, Kubwezera kuli kwanga, Ine ndidzabwezera, ati Ambuye.

20. Koma ngati mdani wako akumva njala, umdyetse, ngati akumva ludzu, ummwetse; pakuti pakutero udzaunjika makala a mota pamutu pace.

21. Musagonje kwa coipa, koma ndi cabwino genietsani coipa.

Aroma 12