Aroma 11:2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Mulungu sanataya anthu ace amene iye anawadziwiratu, Kapena simudziwa kodi cimene lembo linena za Eliya? kuti anaumirira Mulungu poneneza Israyeli, kuti,

Aroma 11

Aroma 11:1-10