Aroma 11:13 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma ndilankhula ndi inu anthu amitundu. Popeza ine ndiri mtumwi wa anthu amitundu, millemekeza utumiki wanga;

Aroma 11

Aroma 11:11-18