Aroma 10:9 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

kuti ngati udzabvomereza m'kamwa mwako Yesu ndiye Ambuye, ndi kukhulupirira mumtima mwako kuti Mulungu anamuukitsa kwa akufa, udzapulumuka:

Aroma 10

Aroma 10:5-19