Aroma 1:9 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pakuti Mulungu ali mboni yanga, amene ndimtumikira mu mzimu wanga, m'Uthenga Wabwino wa Mwana wace, kuti kosalekeza ndikumbukila inu, ndi kupempha masiku onse m'mapemphero anga,

Aroma 1

Aroma 1:5-12