Aroma 1:17 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pakuti m'menemo caonetsedwa cilungamoca Mulungu cakucokera kucikhulupiriro kuloza kucikhulupiriro: monga kwalembedwa, Koma munthu wolungama adzakhala ndi moyo ndi cikhulupiriro.

Aroma 1

Aroma 1:12-21