Amosi 9:3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Angakhale abisala pamwamba pa Karimeli, ndidzawapwaira ndi kuwatenga komweko; angakhale abisala pamaso panga pansi pa nyanja, kumeneko ndidzalamulira njoka, ndipo idzawaluma.

Amosi 9

Amosi 9:1-10