Amosi 9:13 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Taonani akudza masiku, ati Yehova, akud wolima adzapezana ndi wodula, ndi woponda mphesa adzapezana ndi wofesa, ndi mapiri adzakhetsa vinyo watsopano, ndi zitunda zonse zidzasungunuka.

Amosi 9

Amosi 9:11-15