Amosi 7:4 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ambuye Yehova anandionetsa cotere; ndipo taonani, Ambuye Yehova anaitana kuti atsutse ndi moto; ndipo unanyambita cakudya cacikuru ukadanyambitanso dziko.

Amosi 7

Amosi 7:1-12