Pakuti taonani, Yehova walamulira, nadzakantha nyumba yaikuru icite mpata, ndi nyumba yaing'ono icite mindala.