Amosi 3:11 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Cifukwa cace, atero Ambuye Yehova, Padzakhala mdani pozungulira pace pa dziko, nadzatsitsa kukucotsera mphamvu yako; ndi za m'nyumba zako zacifumu adzazifunkha.

Amosi 3

Amosi 3:9-12