Amosi 1:6 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Atero Yehova, Cifukwa ca zolakwa zitatu za Gaza, kapena zinai, sindidzabweza kulanga kwace; popeza anatenga ndende anthu onse kuwapereka kwa Edomu;

Amosi 1

Amosi 1:1-7