Akolose 3:22 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Akapolo inu, mverani m'zonse iwo amene ali ambuye monga mwa thupi, wosati ukapolo wa pamaso, monga okondweretsa anthu, komatu ndi mtima wakulinga kumodzi, akuopa Ambuye;

Akolose 3

Akolose 3:17-25