Akolose 3:1-2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Cifukwa cace ngati munaukitsidwa pamodzi ndi Kristu, funani zakumwamba, kumene kuli Kristu wokhala pa dzanja lamanja la Mulungu.

2. Lingalirani zakumwamba osati za padziko ai.

Akolose 3