Akolose 2:22-23 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

22. (ndizo zonse zakuonongedwa pocita nazo), monga mwa malangizo ndi maphunziro a anthu?

23. zimene ziri naotu manenedwe a nzeru m'kutumikira kwa cifuniro ca mwini wace, ndi kudzicepetsa, ndi kusalabadira thupi; koma ziribe mphamvu konse yakuletsa cikhutitso ca thupi.

Akolose 2