Ahebri 9:15 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo mwa ici ali Nkhoswe ya cipangano catsopano, kotero kuti, popeza kudacitika imfa yakuombola zolakwa za pa cipangano coyamba, oitanidwawo akalandire lonjezano la zolowa zosatha.

Ahebri 9

Ahebri 9:12-21