Ahebri 7:6 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

koma iye amene mawerengedwe a cibadwidwe cace sacokera mwa iwo, anatenga limodzi la magawo khumi kwa Abrahamu, namdalitsa iye amene ali nao malonjezano.

Ahebri 7

Ahebri 7:1-9