Ahebri 7:27 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

amene alibe cifukwa ca kupereka nsembe tsiku ndi tsiku monga akulu a ansembe, yoyambira cifukwa ca zoipa za iwo eni, yinayi cifukwa ca zoipa za anthu; pakuti ici anacita kamodzi, kwatha, podzipereka yekha.

Ahebri 7

Ahebri 7:26-28