Ahebri 7:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pakuti Melikizedeke uyu, Mfumu ya Salemu, wansembe wa Mulungu Wamkulukulu, amene anakomana ndi Abrahamu, pobwera iye adawapha mafumu aja, namdalitsa,

Ahebri 7

Ahebri 7:1-6