Ahebri 6:10 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

pakuti Mulungu sali wosalungama kuti adzaiwala nchito yanu, ndi cikondico mudacionetsera ku dzina lace, umo mudatumikira oyera mtima ndi kuwatumikirabe.

Ahebri 6

Ahebri 6:4-11