Ahebri 5:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pakuti mkulu wa ansembe ali yense, wotengedwa mwa anthu, amaikika cifukwa ca anthu m'zinthu za kwa Mulungu, kuti apereke mitulo, ndiponso nsembe, cifukwa ca macimo:

Ahebri 5

Ahebri 5:1-10