Ahebri 3:18-19 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

18. Ndipo adawalumbirira ayani kuti asalowe mpumulo wace?

19. Si awo kodiosamverawo? Ndipo tiona kuti sanakhoza kulowa cifukwa ca kusakhulupirira.

Ahebri 3