Ahebri 2:14 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Popeza tsono ana ndiwo a mwazi ndi nyama, Iyenso momwemo adalawa nao makhalidwe omwewo kuti mwa imfa akamuononge iye amene anali nayo mphamvu ya imfa, ndiye mdierekezi;

Ahebri 2

Ahebri 2:9-16