Ahebri 13:9 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Musatengedwe ndi maphunzitso a mitundu mitundu, ndi acilendo; pakuti nkokoma kuti mtima ukhazikike ndi cisomo; kosati ndi zakudya, zimene iwo adazitsata sanapindula nazo.

Ahebri 13

Ahebri 13:2-10