Ahebri 13:23-25 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

23. Zindikirani kuti mbale wathu 4 Timoteo wamasulidwa; pamodzi ndi iye, ngati akudza msanga, ndidzakuonani inu.

24. Lankhulani 5 atsogoleri anu onse, ndi oyera mtima onse. Akulankhulani iwo a ku Italiya.

25. Cisomo cikhale ndi inu nonse. Amen.

Ahebri 13