Ahebri 13:1-2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Cikondi ca pa abale cikhalebe.

2. Musaiwale kucereza alendo; pakuti mwa ici ena anacereza angelo osacidziwa.

Ahebri 13