Ahebri 12:25 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Penyani musakane wolankhulayo. Pakuti ngati iwowa sanapulumuka, pomkana iye amene anawacenjeza padziko, koposatu sitidzapulumuka ife, odzipatulira kwa iye wa Kumwamba;

Ahebri 12

Ahebri 12:18-29