Ahebri 12:22 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Komatu mwayandikira ku phiri la Ziyoni, ndi mudzi wa Mulungu wamoyo, Yerusalemu wa Kumwamba, ndi kwa unyinji wocuruka wa angelo,

Ahebri 12

Ahebri 12:17-25