Ahebri 11:6 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

koma wopanda cikhulupiriro sikutheka kumkondweretsa; pakuti iye wakudza kwa Mulungu ayenera kukhulupirira kuti alipo, ndi kuti ali wobwezera mphotho iwo akumfuna iye.

Ahebri 11

Ahebri 11:3-8