Ahebri 11:39-40 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

39. Ndipo iwo onse 21 adacitidwa umboni mwa cikhulupiriro, sanalandira lonjezanolo,

40. 22 popeza Mulungu adatikonzera ife kanthu koposa, kuti iwo asayesedwe amphumphu opanda ife.

Ahebri 11