Ahebri 10:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

mthunzi wa zokoma zirinkudza, osati cifaniziro ceni ceni ca zinthuzo, sicikhozatu, ndi nsembe zomwezi caka ndi caka, zimene azipereka kosalekeza, kuwayesera angwiro iwo akuyandikira.

Ahebri 10

Ahebri 10:1-9