Ahebri 1:5 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pakuti kwa mngelo uti anati nthawi iri yonse,Iwe ndiwe Mwana wanga,Lero ine ndakubala Iwe?ndiponso,Ine ndidzakhala kwa iye Atate,Ndipo iye adzakhala kwa ine Mwana?

Ahebri 1

Ahebri 1:1-8