Agalatiya 4:30-31 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

30. Koma lembo linena ciani? Taya kubwalo mdzakazi ndi mwana wace, pakuti sadzalowa nyumba mwanawa mdzakazi pamodzi ndi mwana wa mfulu.

31. Cifukwa cace, abale, z sitiri ana a mdzakazi, komatu a mfulu.

Agalatiya 4