Agalatiya 4:25 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma Hagara ndiye phiri la Sinai, m'Arabiya, nafanana ndi Yerusalemu wa tsopano; pakuti ali muukapolo pamodzi ndi ana ace.

Agalatiya 4

Agalatiya 4:23-31