Agalatiya 3:8 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo malembo, pakuoneratu kuti Mulungu adzayesa olungama amitundu ndi cikhulupiriro, anayamba kale kulalikira Uthenga Wabwino kwa Abrahamu, kuti, Idzadalitsidwa mwa iwe mitundu yonse.

Agalatiya 3

Agalatiya 3:3-10