Agalatiya 1:12 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pakutitu sindinaulandira kwa munthu, kapena sindinauphunzira, komatu unadza mwa bvumbulutso la Yesu Kristu.

Agalatiya 1

Agalatiya 1:2-14