Afilipi 4:21-23 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

21. Lankhulani woyera mtima ali yense mwa Kristu Yesu. Abalewo akukhala ndiine alankhula inu.

22. Oyera mtima onse alankhula inu, koma makamaka-fwo a banja la Kaisara.

23. Cisomo ca Ambuye Yesu Kristu cikhale ndi mzimu wanu.

Afilipi 4